Chex BT

Chex BT

EstiloPop
Plays330plays
Tamanho
Imprimir

Chex Bt - Ndiwe Wanga (Prod. By Eucalipto Studio)

Composição: Chex BT Madóda.
É o King Chex Haaaaa, the only, the only Ndiwe wekha, iwe wekha, ndiwe wanga Verso 1 Ndiwe wanga, beby yanga, nkazi wanga Baby ine ndimakonda iwe wekha Baby ine ndimafuna iwe wekha Love yanga ndimapatsa iwe wekha... Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga... Iwe ndiwe wanga wanga Future Mother wa ana anga Madamo a nyumba yanga... Ndiwe wekha unatenga Coro Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love 3x) Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love 3x) Verso 2 Padziko assanje alipo ambiri Tiye tikondane m'mene tililj Iwe ndi ine tipangue mbiri...(huuuu mbiri) Opanda iwe sinditha kukhala Opanda iwe baby ine ndimamala Zokamba kamba ossawavela Kukhala ndiwe, baby ine ndimamala Coro Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love 3x) Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga (My love 3x)

319

plays

Comentários

Filtrar Por:
Escreva um comentário

Playlists relacionadas à musica